Zamkatimu
February 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
3 Mbiri ya Moyo Wanga—Yehova Wandithandiza Kwambiri Pomutumikira
MLUNGU WA APRIL 4-10, 2016
8 Abulahamu Anali “Bwenzi” la Yehova
MLUNGU WA APRIL 11-17, 2016
13 Tsanzirani Anthu Amene Anali pa Ubwenzi Wolimba ndi Yehova
Nkhanizi zitithandiza kulimbitsa ubwenzi wathu ndi Yehova. M’nkhani yoyamba tikambirana za chitsanzo cha Abulahamu. M’nkhani yachiwiri tikambirana za Rute, Hezekiya ndiponso Mariya, mayi ake a Yesu.
18 Kodi Mungatani Kuti Muzitumikirabe Yehova Mosangalala?
MLUNGU WA APRIL 18-24, 2016
21 Muzikhala Okhulupirika kwa Yehova
MLUNGU WA APRIL 25, 2016–MAY 1, 2016
26 Tizitsanzira Atumiki a Yehova Amene Anali Okhulupirika
M’nkhanizi tikambirana chitsanzo cha Mfumu Davide komanso cha anthu amene anakhalapo pa nthawi yake. Nkhani zimenezi zitithandiza kuona mmene mfundo za m’Baibulo zingatithandizire kukhala okhulupirika kwa Yehova pa zinthu zosiyanasiyana.
31 Kale Lathu
CHITHUNZI CHA PACHIKUTO:
BENIN
M’mudzi wa Hétin, anthu ambiri amamanga nyumba zawo paphaka ndipo amagwiritsa ntchito mabwato akafuna kupita kwinakwake. M’mudziwu muli mipingo itatu, ofalitsa 215 komanso apainiya 28. N’zosangalatsa kuti mu 2014, anthu okwana 1,600 anapezeka pa Chikumbutso
KULI ANTHU
10,703,000
KULI OFALITSA
12,167
KULI APAINIYA OKHAZIKIKA