Magazini Yophunzira
JUNE 2016
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: AUGUST 1 MPAKA 28, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
TRINIDAD
Anthu ambiri a ku Trinidad ndi ku Tobago amakonda kusodza m’mbali mwa nyanja. A Mboni za Yehova amayesetsa kulalikira kwa asodziwa
KULI OFALITSA
9,679
MAPHUNZIRO A BAIBULO
11,331
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2015)
24,103
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.