Magazini Yophunzira
DECEMBER 2016
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA JANUARY 30 MPAKA FEBRUARY 26, 2017
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
PORTUGAL
Anthu ambiri amapita mumzinda wa Aveiro womwe uli kumpoto kwa dzikoli kukaona madamu ochititsa chidwi opangira mchere. A Mboni akumeneku amalalikira uthenga wabwino kwa anthu amene amagulitsa mcherewo
OFALITSA
48,840
MAPHUNZIRO A BAIBULO
28,687
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2015)
91,472
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka, pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.