Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
MLUNGU WA APRIL 3-9, 2017
3 Cholinga cha Yehova Chidzakwaniritsidwa
MLUNGU WA APRIL 10-16, 2017
8 Dipo Ndi ‘Mphatso Yangwiro’ Yochokera kwa Atate
Dipo la Khristu ndi lofunika kwambiri pa chikhulupiriro chathu. Limathandizanso kwambiri kuti cholinga cha Mulungu chokhudza anthu chidzakwaniritsidwe. Nkhani ziwirizi zikufotokoza chifukwa chake panafunika dipo, zimene linakwaniritsa komanso zimene tingachite posonyeza kuti timayamikira mphatso yamtengo wapatali imeneyi.
13 Mbiri ya Moyo Wanga—Mulungu Anatisonyeza Kukoma Mtima Kwakukulu M’njira Zambiri
MLUNGU WA APRIL 17-23, 2017
18 Yehova Amatsogolera Anthu Ake
MLUNGU WA APRIL 24-30, 2017
23 Kodi Ndi Ndani Akutsogolera Anthu a Mulungu Masiku Ano?
Yehova wakhala akusankha anthu kuti azitsogolera anthu ake. Kodi tikudziwa bwanji kuti Yehova amathandiza anthu amenewa komanso kapolo wokhulupirika masiku ano? Nkhani ziwirizi zikufotokoza zinthu zitatu zomwe zimatithandiza kudziwa anthu amene Mulungu akuwagwiritsa ntchito.
29 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
31 Kale Lathu