Magazini Yophunzira
January 2018
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: FEBRUARY 26–APRIL 1, 2018
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
BOLIVIA
Mabanja awiri a apainiya m’tauni ya Riberalta ku Beni akupakira mabuku mundege n’cholinga choti akalalikire kudera lakutali kwambiri m’dzikolo
KULI OFALITSA
26,081
MAPHUNZIRO A BAIBULO
42,568
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2016)
75,027
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.pr2711.com/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.