Magazini Yophunzira
OCTOBER 2018
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: DECEMBER 3-30, 2018
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
VENEZUELA
Mayi ali mu utumiki ndi ana ake mumzinda wa Caracas ndipo wawagulira zakumwa zoziziritsa kukhosi
KULI OFALITSA
149,355
MAPHUNZIRO A BAIBULO
209,866
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2017)
478,266
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo
Ngati mukufuna kupereka, pitani pawebusaiti yathu ya www.pr2711.com/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.