Magazini Yophunzira
NOVEMBER 2018
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: DECEMBER 31, 2018–FEBRUARY 3, 2019
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
SWEDEN
Ofalitsa ku Stockholm akulalikira madzulo chifukwa choti pa nthawiyi kwawoko dzuwa sililowa msanga. Akulalikira kwa madalaivala, ogulitsa m’masitolo, ogulitsa mafuta ndi anthu ena ogwira ntchito usiku
KULI OFALITSA
22,418
MAPHUNZIRO A BAIBULO
10,027
OPEZEKA PACHIKUMBUTSO (2017)
34,966
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka, pitani pawebusaiti yathu ya www.pr2711.com/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.