Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
MLUNGU WA FEBRUARY 4-10, 2019
Akhristu oona amayembekezera kwambiri kudzakhala m’paradaiso. Nkhaniyi ikufotokoza mfundo za m’Malemba zotithandiza kuyembekezera zimenezi komanso tanthauzo la lonjezo la Yesu lokhudza paradaiso.
8 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
MLUNGU WA FEBRUARY 11-17, 2019
10 Tizilemekeza “Chimene Mulungu Wachimanga Pamodzi”
Nkhaniyi ikufotokoza zimene Baibulo limanena pa nkhani ya kulemekeza ukwati. Kodi tingasonyeze bwanji kuti timalemekeza ukwati? Nanga tingatsatire bwanji zimene Baibulo limanena pa nkhani ya kuthetsa banja komanso kupatukana?
15 Mbiri ya Moyo Wanga—‘Yehova Watichitira Zinthu Zabwino’
MLUNGU WA FEBRUARY 18-24, 2019
19 Achinyamata, Mlengi Wanu Amafuna Kuti Muzikhala Osangalala
MLUNGU WA FEBRUARY 25, 2019–MARCH 3, 2019
24 Achinyamata, Mukhoza Kukhala ndi Moyo Wosangalala
Nthawi zambiri achinyamata amafunika kusankha zochita pa nkhani zikuluzikulu monga zimene angachite pa moyo wawo. Aphunzitsi komanso akuluakulu ena m’dzikoli amalimbikitsa anthu kuti azifunafuna maphunziro apamwamba komanso ntchito yabwino. Koma Yehova amalimbikitsa achinyamata kuti aziika kumutumikira pamalo oyamba. Nkhani ziwirizi zikusonyeza kuti ndi nzeru kumvera Mulungu.
29 “Wolungama Adzakondwera mwa Yehova”
32 Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2018