Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp19 No. 1 tsamba 1-2
  • Kodi Mulungu Ndi Ndani?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mulungu Ndi Ndani?
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2019
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2019
wp19 No. 1 tsamba 1-2
Magazini ya Nsanja ya Olonda, Na. 1, 2019 | Kodi Mulungu Ndi Ndani?

Kodi Mulungu Ndi Ndani?

© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka ndalama, pitani pa www.jw.org. Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.

MAGAZINI ya Nsanja ya Olonda imalemekeza Yehova Mulungu, yemwe ndi Wolamulira wa chilengedwe chonse. Imalimbikitsa anthu ndi uthenga wabwino wakuti posachedwapa Ufumu wa Mulungu uchotsa zoipa zonse n’kusintha dziko lapansili kukhala Paradaiso. Imalimbikitsanso anthu kukhulupirira Yesu Khristu yemwe anatifera kuti tidzapeze moyo wosatha ndipo panopo akulamulira monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Magaziniyi yakhala ikufalitsidwa kuyambira mu 1879 ndipo si yandale. Mfundo zake zimachokera m’Baibulo.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena