Nkhani Zimene Zatuluka Pa Jw Library Komanso Jw.Org
KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
Luso la Dolphin Lozindikira Zinthu Mosavuta
Asayansi akuyesetsa kutengera luso la nyamazi kuti apange zipangizo zowathandiza kufufuza ndiponso kuzindikira zimene zili m’madzi.
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > WAS IT DESIGNED?
Pa jw.org pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > BAIBULO KOMANSO SAYANSI > KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Mungathandize Bwanji Mwana Wanu Kuti Azikhoza Bwino Kusukulu?
Mwana akamapanikizika, amakhala ndi nkhawa kusukulu ndiponso kunyumba. Makolo ayenera kuzindikira chifukwa chake mwana wawo sakukhoza bwino n’kumamulimbikitsa.
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > HELP FOR THE FAMILY.
Pa jw.org pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA > KULERA ANA.