Nkhani Zimene Zatuluka Pa JW Library komanso JW.ORG
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Mmene Mungathandizire Ana Anu pa Nkhani ya Mowa
Kodi makolo ayenera kuthandiza bwanji ana awo pa nkhani ya mowa ndipo ayenera kuchita zimenezi liti?
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > HELP FOR THE FAMILY.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA > KULERA ANA.
KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
Khungu la Nangumi Lotha Kudziyeretsa Lokha
N’chifukwa chiyani asayansi akufuna kutsanzira zimene khungu la nangumi limachita?
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > WAS IT DESIGNED?
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti BAIBULO KOMANSO SAYANSI > KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?