Magazini Yophunzira
OCTOBER 2019
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: DECEMBER 2-29, 2019
© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
PATSAMBA LOYAMBA:
Posachedwapa, Yesu adzatsogolera magulu a asilikali akumwamba pomenya nkhondo ya Aramagedo kuti awononge adani a Mulungu (Onani nkhani yophunzira 41, ndime 17)