Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 6/95 tsamba 7
  • Zilengezo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zilengezo
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—1995
Utumiki Wathu wa Ufumu—1995
km 6/95 tsamba 7

Zilengezo

◼ Mabuku ogaŵira mu June: Baibulo—Kodi Ndilo Mawu a Mulungu Kapena a Munthu? July ndi August: Lililonse la mabrosha otsatirawa a masamba 32 lingagwiritsiridwe ntchito: Boma Limene Lidzabweretsa Paradaiso, Dzina la Mulungu Limene Lidzakhala Kosatha, Kodi Chifuno cha Moyo Nchiyani—Kodi Mungachipeze Motani?, Kodi Mulungu Amatisamaliradi?, Kodi Muyenera Kukhulupirira Utatu?, Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira, Sangalalani ndi Moyo pa Dziko Lapansi Kosatha!, ndi “Tawonani! Ndikupanga Zinthu Zonse Zatsopano.” September: Buku la Kukhala ndi Moyo Kosatha lidzagwiritsiridwa ntchito, ndipo payenera kukhala kuyesayesa kwa kuyambitsa maphunziro a Baibulo apanyumba. CHIDZIŴITSO: Mipingo imene sinaodebe zinthu zamkupiti zotchulidwa pamwambapa iyenera kutero pa fomu yawo ya Literature Request (S-AB-14) yotsatira ya mwezi ndi mwezi.

◼ Woyang’anira wotsogoza kapena wina woikidwa ndi iye ayenera kuŵerengera maakaunti a mpingo pa June 1 kapena mwamsanga pambuyo pake. Lengezani ku mpingo mutachita zimenezi.

◼ Kuyambira m’June, mabaji a msonkhano wachigawo wa 1995 adzatumizidwa ku mipingo yonse. Simudzafunikira kuwaodetsa. Malinga ndi ukulu wa mpingo uliwonse, mabaji adzatumizidwa m’maunyinji a 25. Muyenera kuodetsa zoikamo zake zapulasitiki za aliyense amene akuzifuna mumpingo.

◼ Zofalitsa Zomwe Zilipo:

Watch Tower Publications Index 86-90; mabaundi voliyumu a Watchtower ndi Awake a 1994—Chingelezi

◼ Ma Compact Disc Atsopano Omwe Alipo:

Sing Praises to Jehovah on Compact Disc (seti ya ma disc asanu ndi atatu)—Chingelezi

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena