Phunziro la Buku la Mpingo
Ndandanda ya maphunziro a mpingo m’bolosha lakuti “Tawonani! Ndikupanga Zinthu Zonse Zatsopano.”
December 7: Ndime 51 mpaka 58 ndi Mafunso Obwereza 12
Ndandanda ya maphunziro a mpingo m’bolosha lakuti Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira.
December 14: tsa. 03 mpaka tsa. 06
December 21: tsa. 07 mpaka tsa. 11*
December 28: tsa. 11* mpaka tsa. 13
*Kulekezera kapena kuyambira pakamutu.