Zilengezo
◼ Mabuku ogaŵira mu June: Phunzirani kwa Mphunzitsi Waluso. Ngati anthu anena kuti alibe ana, gaŵirani bulosha la Mulungu Amafunanji. Pogwiritsa ntchito buloshali, yesetsani kuyambitsa maphunziro a Baibulo apanyumba. July ndi August: Mabulosha alionse amene mpingo uli nawo. September: Chinsinsi cha Chimwemwe cha Banja.