Zochitika mu Utumiki Wakumunda
Mu October 2013, tinachititsa maphunziro a Baibulo okwana 104,121. Zimenezi zikusonyeza kuti padakali anthu ambiri ofunika kuphunzira choonadi kuti adziwe Yehova Mulungu. Choncho tiyeni tipitirize kuthandiza anthu amenewa kuti apite patsogolo mwauzimu.