Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 July tsamba 2
  • July 4-10

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 4-10
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 July tsamba 2

July 4-10

MASALIMO 60-68

  • Nyimbo Na. 104 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tamandani Yehova Wakumva Pemphero”: (10 min.)

    • Sal. 61:1, 8​—Muzipempha Yehova kuti akuthandizeni kukwaniritsa zomwe munamulonjeza (w99 9/15 9 ndime 1-4; w08 2/15 7 ndime 3)

    • Sal. 62:8​—Muzisonyeza kuti mumakhulupirira Yehova pomuuza zakukhosi kwanu (w15 4/15 25-26 ndime 6-9)

    • Sal. 65:1, 2​—Yehova amamva mapemphero a anthu a mitima yabwino (w15 4/15 22 ndime 13-14; w10 4/15 5 ndime 10; it-2-E 668 ndime 2)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Sal. 63:3​—N’chifukwa chiyani kukoma mtima kwa Yehova n’kwabwino kuposa moyo? (w06 6/1 11 ndime 9)

    • Sal. 68:18​—Kodi ndani amene anali “mphatso za amuna”? (w06 6/1 10 ndime 5)

    • Kodi ndaphunzira chiyani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 63:1–64:10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Konzekerani Zitsanzo za Ulaliki za Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani kavidiyo kosonyeza zitsanzo za ulaliki kenako kambiranani mfundo zimene tikuphunzirapo. Limbikitsani omvera kuti alembe ulaliki umene angakonde kugwiritsa ntchito.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 81

  • “Tizikhala Moyo Wosalira Zambiri Kuti Titumikire Bwino Mulungu”: (15 min.) Yambani ndi kukambirana nkhaniyi. Kenako onerani vidiyo ya pa JW Broadcasting ya mutu wakuti, Timakhala Moyo Wosalira Zambiri ndipo kenako kambiranani zimene tikuphunzirapo. (Pitani pamene alemba kuti MAVIDIYO ENA > BANJA.) Pomaliza, limbikitsani onse kuti ayesetse kumakhala moyo wosalira zambiri kuti azitumikira Yehova popanda chosokoneza chilichonse.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 1 ndime 14-27 ndi Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 16.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 88 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena