Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 July tsamba 6
  • July 18-24

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 18-24
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 July tsamba 6

July 18-24

MASALIMO 74-78

  • Nyimbo Na. 110 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tizikumbukira Ntchito za Yehova”: (10 min.)

    • Sal. 74:16; 77:6, 11, 12​—Tiziganizira ntchito za Yehova (w15 8/15 10 ndime 3-4; w04 3/1 19-20; w03 7/1 10 ndime 6-7)

    • Sal. 75:4-7​—Ntchito ina imene Yehova amagwira ndi kusankha amuna oti azitsogolera mumpingo (w06 7/15 11 ndime 3; it-1-E 1160 ndime 7)

    • Sal. 78:11-17​—Tizikumbukira mmene Yehova wakhala akupulumutsira atumiki ake (w04 4/1 21-22)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Sal. 78:2​—Kodi lembali linakwaniritsidwa bwanji kudzera mwa Mesiya? (w11 8/15 11 ndime 14)

    • Sal. 78:40, 41​—Mogwirizana ndi mavesi amenewa, kodi zochita zathu zingakhudze bwanji Yehova? (w12 11/1 14 ndime 5; w11 7/1 10)

    • Kodi ndaphunzira chiyani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 78:1-21

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp16.4 tsamba 16​—Muuzeni kuti akhoza kupereka ndalama zothandizira ntchito yolalikira ngati akufuna.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp16.4 tsamba 16

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 5 ndime 6 ndi 7

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 15

  • Zofunika pampingo: (10 min.)

  • “Yehova . . . Analenga Zinthu Zonse”: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi yomwe imapezeka pa webusaiti ya jw.org/ny yakuti “Yehova . . . Analenga Zinthu Zonse.” (Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA.) Mukamaliza, itanani ana angapo kuti abwere kutsogolo ndipo afunseni mafunso okhudza vidiyoyi.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 2 ndime 13-23

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena