Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 October tsamba 3
  • October 10-16

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 10-16
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 October tsamba 3

October 10-16

MIYAMBO 7-11

  • Nyimbo Na. 32 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mtima Wako Usapatuke”: (10 min.)

    • Miy. 7:6-12—Nthawi zambiri anthu opanda nzeru amachita zinthu zimene zingasokoneze ubwenzi wawo ndi Yehova (w00 11/15 29-30)

    • Miy. 7:13-23—Munthu akasankha zinthu mopanda nzeru akhoza kukumana ndi mavuto aakulu (w00 11/15 30-31)

    • Miy. 7:4, 5, 24-27—Tikakhala anzeru komanso omvetsa zinthu tidzapewa mavuto ambiri (w00 11/15 29, 31)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Miy. 9:7-9—Kodi zimene timachita tikapatsidwa malangizo zimasonyeza kuti ndife anthu otani? (w01 5/15 29-30)

    • Miy. 10:22—Kodi ndi madalitso ati amene Yehova akutipatsa masiku ano? (w06 5/15 26-30 ndime 3-16)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Miy. 8:22-36; 9:1-6

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Nkhani yokhudza mutu wapachikuto wa g16.5—Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Nkhani yokhudza mutu wapachikuto wa g16.5—Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 186-187 ndime 5-6—Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 83

  • Zimene Achinyamata Anzanu Amanena—Foni Zam’manja (Miy. 10:19): (15 min.) Nkhani yokambirana. Poyamba, onetsani vidiyo yakuti, Zimene Achinyamata Anzanu Amanena—Foni Zam’manja. Kenako kambiranani nkhani ya pa jw.org/ny yakuti, “Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani Zokhudza Mameseji a Pafoni?” Fotokozani bwino mfundo zomwe zili pakamutu kakuti, “Zofunika Kukumbukira pa Nkhani ya Mameseji.”

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 8 ndime 17-27 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 75.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 152 ndi Pemphero

    Kumbukirani: Muyenera kuika nyimboyi kuti onse amvetsere, kenako muibwerezenso kuti onse aimbe nawo.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena