Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 October tsamba 4
  • October 17-23

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 17-23
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 October tsamba 4

October 17-23

MIYAMBO 12-16

  • Nyimbo Na. 69 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Nzeru Ndi Yabwino Kuposa Golide”: (10 min.)

    • Miy. 16:16, 17—Munthu wanzeru amaphunzira Mawu a Mulungu komanso kuwagwiritsa ntchito (w07 7/15 8)

    • Miy. 16:18, 19—Munthu wanzeru amapewa kunyada ndiponso kudzikuza (w07 7/15 8-9)

    • Miy. 16:20-24—Munthu wanzeru amalankhula zinthu zothandiza ena (w07 7/15 9-10)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Miy. 15:15—Kodi tingatani kuti tizisangalala kwambiri pa moyo wathu? (g 11/13 16)

    • Miy. 16:4—Kodi Yehova angagwiritse ntchito bwanji anthu oipa kuti akwaniritse zolinga zake? (w07 5/15 18-19)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Miy. 15:18-33; 16:1-6

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yoh. 11:11-14—Kuphunzitsa Choonadi. Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Gen. 3:1-6; Aroma 5:12—Kuphunzitsa Choonadi. Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 202 ndime 18-19—Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 117

  • “Zimene Tingachite Kuti Ndemanga Zathu Zizikhala Zabwino”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Poyamba, onetsani vidiyo yakuti, Khalani Bwenzi la Yehova—Uzikonzekera Zimene Ukayankhe. Kenako pemphani ana amene munawasankhiratu kuti abwere kupulatifomu ndipo muwafunse mafunso awa: Kodi muyenera kuchita zinthu 4 ziti pokonzekera ndemanga? N’chifukwa chiyani tingakhalebe osangalala ngakhale kuti sitinapatsidwe mwayi woyankha pamisonkhano?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 9 ndime 1-13

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 102 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena