Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 October tsamba 7
  • October 31–November 6

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 31–November 6
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 October tsamba 7

October 31–November 6

MIYAMBO 22-26

  • Nyimbo Na. 88 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Phunzitsa Mwana M’njira Yomuyenerera” (10 min.)

    • Miy. 22:6; 23:24, 25—Makolo akamaphunzitsa ana pogwiritsa ntchito mfundo za m’Baibulo, nthawi zambiri anawo akakula amakhala osangalala ndiponso odalirika (w08 4/1 16; w07 6/1 31)

    • Miy. 22:15; 23:13, 14—M’lembali, “ndodo” imaimira kuphunzitsa, kulangiza komanso kupereka chilango (w15 11/15 5 ndime 6; w07 2/15 27 ndime 18; w97 10/15 32; it-2-E 818 ndime 4)

    • Miy. 23:22—Ngakhale Ana atakula, akhoza kupindula ndi nzeru za makolo awo (w04 6/15 14 ndime 1-3; w00 6/15 21 ndime 13)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza (8 min.)

    • Miy. 24:16—Kodi lembali limatilimbikitsa bwanji kuti tizipirira pa mpikisano wokalandira moyo wosatha? (w13 3/15 4-5 ndime 5-8)

    • Miy. 24:27—Kodi lembali lili ndi mfundo yotani? (w09 10/15 12 ndime 1)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Miy. 22:1-21

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Khadi lodziwitsa anthu za JW.ORG—Kulalikira mwamwayi.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Khadi lodziwitsa anthu za JW.ORG—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane mukadzabweranso. Pomaliza, muuzeni kuti mukufuna kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo?

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 179-181 ndime 18-19

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 101

  • “Kodi Mukugwiritsa Ntchito Bwino Makadi Odziwitsa Anthu za JW.ORG?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Poyamba, onetsani vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki, kenako kambiranani mfundo zimene tikuphunzirapo. Limbikitsani ofalitsa kuti azinyamula makadiwa nthawi zonse.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 10 ndime 1-11, bokosi patsamba 86.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 146 ndi Pemphero

    Kumbukirani: Muyenera kuika nyimboyi kuti onse amvetsere, kenako muibwerezenso kuti onse aimbe nawo.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena