Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 November tsamba 2
  • November 7-13

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 7-13
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 November tsamba 2

November 7-13

MIYAMBO 27-31

  • Nyimbo Na. 86 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Baibulo Limafotokoza Zimene Mkazi Wabwino Amachita”: (10 min.)

    • Miy. 31:10-12—Amakhala wodalirika (w15 1/15 20 ndime 10; w00 2/1 31 ndime 2; it-2-E 1183)

    • Miy. 31:13-27—Amakhala wakhama ndiponso wanzeru (w00 2/1 31 ndime 3-4)

    • Miy. 31:28-31—Amakonda Yehova ndipo anthu amamulemekeza (w15 1/15 20 ndime 8; w00 2/1 31 ndime 5, 8)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Miy. 27:12—Kodi tingakhale bwanji ochenjera pa nkhani yosankha zosangalatsa? (w15 7/1 8 ndime 3)

    • Miy. 27:21—Kodi munthu angayesedwe bwanji ndi “chitamando” chimene walandira? (w11 8/1 29 ndime 1; w06 9/15 19 ndime 12)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Miy. 29:11-27; 30:1-4

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Pambuyo poonetsa vidiyo iliyonse ya chitsanzo cha ulaliki, kambiranani mfundo zimene tikuphunzirapo. Limbikitsani ofalitsa kuti azilemba ulaliki wawowawo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 89

  • “Mwamuna Wake Amadziwika Pazipata”: (5 min.) Nkhani yokambidwa ndi mkulu.

  • Zofunika Pampingo: (10 min.) Mukhozanso kukambirana mfundo zimene tikuphunzira mu Buku Lapachaka. (yb16 40-41)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 10 ndime 12-21 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 91

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 108 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena