Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 February tsamba 4
  • February 20-26

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 20-26
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 February tsamba 4

February 20-26

YESAYA 58-62

  • Nyimbo Na. 142 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tikalengeze za Chaka cha Yehova Chokomera Anthu Mtima”: (10 min.)

    • Yes. 61:1, 2​—Yesu anadzozedwa kuti ‘alengeze chaka cha Yehova chokomera anthu mtima’ (ip-2 322 ¶4)

    • Yes. 61:3, 4​—Yehova amatipatsa “mitengo ikuluikulu ya chilungamo” kuti izitithandiza pa ntchito yake (ip-2 326-327 ¶13-15)

    • Yes. 61:5, 6​—“Anthu ochokera kwina” amagwirizana ndi “ansembe a Yehova” pogwira ntchito yaikulu yolalikira padziko lonse (w12 12/15 25 ¶5-6)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yes. 60:17​—Kodi Yehova wakwaniritsa bwanji lonjezoli m’masiku otsiriza ano? (w15 7/15 9-10 ¶14-17)

    • Yes. 61:8, 9​—Kodi “pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale” n’chiyani, nanga “ana” ndi ndani? (w07 1/15 11 ¶6)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 62:1-12

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.1 chikuto

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.1 chikuto

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 15 ¶19​—Ngati n’zotheka, chitsanzochi chikhale cha mayi akuphunzira ndi mwana wake wamkazi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 47

  • Muzigwiritsa Ntchito Mavidiyo mu Utumiki: (6 min.) Nkhani. Onetsani vidiyo yakuti Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani? Limbikitsani abale ndi alongo kugwiritsa ntchito vidiyoyi mu March ndi April pokambirana ndi anthu pa ulendo woyamba kapena wobwereza.

  • “Tizigwiritsa Ntchito Mwanzeru Mabuku Ndiponso Magazini”: (9 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Ntchito Yotumiza Mabuku ku Congo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 18 ¶1-13

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 114 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena