July 3-9
EZEKIELI 11-14
Nyimbo Na. 52 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Muli ndi Mtima Wofewa Ngati Mnofu?”: (10 min.)
Ezek. 11:17, 18—Yehova analonjeza kuti adzabwezeretsa kulambira koona (w07 7/1 11 ¶4)
Ezek. 11:19—Yehova angatipatse mtima woti tizimvera malamulo ake (w16.05 15 ¶9)
Ezek. 11:20—Yehova amafuna kuti tizigwiritsa ntchito zimene timaphunzira
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Ezek. 12:26-28—Kodi mavesiwa akusonyeza kuti atumiki a Yehova ali ndi udindo wotani? (w07 7/1 13 ¶8)
Ezek. 14:13, 14—Kodi tikuphunzira chiyani pa kutchulidwa kwa anthu atatu amene ali m’mavesiwa? (w16.05 26 ¶13; w07 7/1 13 ¶9)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 12:1-10
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Kukambirana “Zitsanzo za Ulaliki.” Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.) Mukhoza kukambirana mfundo zimene tikuphunzira mu Buku Lapachaka. (yb17 41-43)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 3 ¶1-12, komanso tsamba 30-31
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 43 ndi Pemphero