Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 October tsamba 2
  • October 2-8

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 2-8
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 October tsamba 2

October 2-8

DANIELI 7-9

  • Nyimbo Na. 116 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Ulosi wa Danieli Unaneneratu Nthawi Imene Mesiya Adzafike”: (10 min.)

    • Dan. 9:24​—Nsembe ya Mesiya inathandiza kuti machimo a anthu akhululukidwe (it-2 902 ¶2)

    • Dan. 9:25​—Mesiya anafika kumapeto kwa mlungu wa 69 wa milungu yoimira zaka (it-2 900 ¶7)

    • Dan. 9:26, 27a​—Mesiya anaphedwa pakatikati pa mlungu wa 70 wa milungu yoimira zaka (it-2 901 ¶2, 5)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Dan. 9:24​—Kodi kudzoza “Malo Opatulikitsa” kunachitika liti? (w01 5/15 27)

    • Dan. 9:27​—Kodi ndi pangano lotani limene anasungira anthu ambiri mpaka kumapeto kwa mlungu wa 70 wa milungu yoimira zaka, kapena kuti mu 36 C.E.? (w07 9/1 20 ¶4)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Dan. 7:1-10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Kukambirana “Zitsanzo za Ulaliki.” Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo. Limbikitsani ofalitsa kuti aziyesetsa kubwerera mwamsanga kwa anthu amene anasonyeza chidwi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 94

  • “Kodi Tingatani Kuti Tiziphunzira Malemba Mwakhama?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Zinthu Zotithandiza Pofufuza Chuma cha M’mawu a Mulungu.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 7 ¶19 mpaka mutu 8 ¶7, komanso tsamba 75, 76-77, 79

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 53 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena