Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 January tsamba 3
  • January 8-14

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 8-14
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 January tsamba 3

January 8-14

MATEYU 4-5

  • Nyimbo Na. 82 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Tikuphunzira pa Zomwe Yesu Anaphunzitsa pa Ulaliki Wapaphiri”: (10 min.)

    • Mat. 5:3​—Munthu amakhala wosangalala ngati amazindikira zosowa zake zauzimu (“Odala (osangalala kapena achimwemwe)” “anthu amene amazindikira zosowa zawo zauzimu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 5:3, nwtsty)

    • Mat. 5:7​—Munthu amakhala wosangalala akamasonyeza ena chifundo (“achifundo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 5:7, nwtsty)

    • Mat. 5:9​—Munthu amasangalala akamakhala mwamtendere ndi ena (“amene amabweretsa mtendere” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 5:9, nwtsty; w07 12/1 17)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Mat. 4:9​—Kodi Satana anayesa Yesu pomuuza kuti achite chiyani? (“kundiweramira kamodzi kokha” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 4:9, nwtsty)

    • Mat. 4:23​—Kodi Yesu ankagwira ntchito ziwiri ziti zomwe ndi zofunika kwambiri? (“kuphunzitsa . . . kulalikira” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 4:23, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 5:31-48

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Onani chitsanzo cha ulaliki.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w16.03 31-32—Mutu: Kodi Satana Anapitadi ndi Yesu Kukachisi Kapena Anangomuonetsa Masomphenya?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 130

  • Odala Ndi Anthu Amene Akuzunzidwa Chifukwa cha Chilungamo: (9 min.) Onetsani vidiyo yakuti Banja la a Namgung: Anamangidwa Chifukwa cha Chikhulupiriro Chawo, kenako kambiranani zimene tikuphunzira m’vidiyoyi.

  • “Kodi Tingatsatire Bwanji Malangizo Akuti Ukayanjane Ndi M’bale Wako Choyamba?”: (6 min.) Nkhani yokambirana. Kambiranani chifukwa chake mfundo yothera iliyonse m’mabokosi awiriwo ili yolondola.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 12 ¶16-23, bokosi patsamba 125, 128 ndi 129

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 141 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena