Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 July tsamba 7
  • Mwana Wolowerera

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mwana Wolowerera
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • “Yehova, Mulungu Wachifundo ndi Wachisomo”
    Nsanja ya Olonda—1998
  • Tsanzirani Chifundo cha Yehova
    Nsanja ya Olonda—1998
  • Kodi Mwana “Wosakaza” Mungamuthandize Bwanji?
    Nsanja ya Olonda—2001
  • Vidiyo Yatsopano Yothandiza Poyambitsa Maphunziro a Baibulo
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 July tsamba 7
David wabwerera ndipo wakumbatirana ndi a bambo ake

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Mwana Wolowerera

ONERANI VIDIYO YAKUTI MWANA WOLOWERERA, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kodi ndi zinthu ziti zimene zikusonyeza kuti David anali atayamba kuyenda m’njira yolakwika, nanga akulu komanso anthu a m’banja lake anachita chiyani poyesetsa kumuthandiza?

  • N’chifukwa chiyani M’bale ndi Mlongo Barker ali chitsanzo chabwino kwa makolo?

  • Kodi taphunzira chiyani m’vidiyoyi pa nkhani ya . . .

    • David ndi Allan ali ku ntchito

      kudzipereka kwambiri pa ntchito yathu?

    • David ndi Allan ali kumalo omwera mowa ndi Vivian ndi Taylor

      kucheza ndi anthu oipa?

    • David akumvetsera pamene a bambo ake akumupatsa malangizo a m’Baibulo

      kumvera malangizo?

    • A John Barker akulankhula ndi mwana wawo wamkulu, James

      kukhululukira anthu amene alapa?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena