Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 August
  • August 27–September 2

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 27–September 2
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 August

August 27–September 2

Luka 23-24

  • Nyimbo Na. 130 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzikhala Okonzeka Kukhululukira Ena”: (10 min.)

    • Luka 23:34​—Yesu anakhululukira asilikali achiroma amene anamupachika (cl 297 ¶16)

    • Luka 23:43​—Yesu anakhululukira chigawenga (g 2/08 11 ¶5-6)

    • Luka 24:34​—Yesu anakhululukira Petulo (cl 297-298 ¶17-18)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Luka 23:31​—Kodi n’kutheka kuti Yesu ankatanthauza chiyani pavesili? (“pamene mtengo uli wauwisi, . . . mtengowo ukadzauma” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 23:31, nwtsty)

    • Luka 23:33​—Kodi pali umboni wotani wosonyeza kuti misomali inkagwiritsidwa ntchito popachika munthu pamtengo? (“Msomali M’fupa Lachidendene” zithunzi ndi mavidiyo pa Luka 23:33, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 23:1-16

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha zimene tinganene. Kenako gawirani buku kapena chilichonse chimene chili m’gulu la Zinthu Zomwe Timagwiritsa Ntchito Pophunzitsa, chomwe chili ndi nkhani yomwe ingathandize mwininyumbayo.

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse ndipo gawirani buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 4 ¶3-4

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 20

  • “Yesu Anaferanso M’bale Wakoyo”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muziona Zinthu Moyenera.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 2

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena