Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 February tsamba 2
  • February 4-10

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 4-10
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 February tsamba 2

February 4-10

AROMA 1-3

  • Nyimbo Na. 88 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Pitirizani Kuphunzitsa Chikumbumtima Chanu”: (10 min.)

    • [Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Aroma.]

    • Aroma 2:14, 15​—Aliyense ali ndi chikumbumtima (lv 16 ¶6)

    • Aroma 2:15​—Tiyenera kuphunzitsa chikumbumtima chathu kuti chizitithandiza kusankha zinthu moyenera (lv 17-18 ¶8-9)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Aroma 3:4​—Kodi timalola kuti “Mulungu akhale wonena zoona” m’njira yotani? (w08 6/15 30 ¶5)

    • Aroma 3:24, 25​—Kodi “dipo lolipiridwa ndi Khristu Yesu” limaphimba bwanji “machimo amene anachitika kale” dipolo lisanaperekedwe? (w08 6/15 29 ¶6)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aroma 1:1-17 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kulankhulana Mokambirana ndi Anthu, kenako kambiranani phunziro 2 m’kabuku ka Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (Osapitirira 5 min) w06 6/1 12-13​—Mutu: Tizikumbukira Kuti Pali Zinthu Zina Zimene Ifeyo Kapena Ena Sangathe Kuchita. (th phunziro 7)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 6

  • “Kodi Mumaona Makhalidwe a Mulungu Osaoneka ndi Maso?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Zachilengedwe Zimatiphunzitsa za Ulemerero wa Mulungu​—Kuwala Komanso Mitundu ya Zinthu.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 24

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 58 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena