Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 April tsamba 3
  • April 8-14

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 8-14
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 April tsamba 3

April 8-14

1 AKORINTO 10-13

  • Nyimbo Na. 30 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova ndi Wokhulupirika”: (10 min.)

    • 1 Akor. 10:13​—Yehova samachita kusankha mayesero oti tingakumane nawo (w17.02 29-30)

    • 1 Akor. 10:13​—Mayesero amene timakumana nawo ndi amenenso “amagwera anthu ena”

    • 1 Akor. 10:13​—Yehova angatithandize kupirira mayesero alionse tikamamudalira

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • 1 Akor. 10:8​—N’chifukwa chiyani vesili limanena kuti Aisiraeli amene anaphedwa tsiku limodzi chifukwa chochita dama analipo 23,000 pomwe pa Numeri 25:9 pamati analipo 24,000? (w04 4/1 29)

    • 1 Akor. 11:5, 6, 10​—Kodi mlongo ayenera kuvala chinachake kumutu akamachititsa phunziro ali ndi m’bale amene ndi wofalitsa? (w15 2/15 30)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 1 Akor. 10:1-17 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri. (th phunziro 3)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Musonyezeni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 6)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 25

  • ‘Ziwalo Zonse za Thupi ndi Zofunika’ (1 Akor. 12:22): (10 min.) Onerani vidiyoyi.

  • “Kodi Muchikonzekera Bwanji Chikumbutso?”: (5 min.) Nkhani. Limbikitsani onse kugwiritsa ntchito nyengo ya Chikumbutsoyi kuganizira za kufunika kwa mwambowu ndiponso chikondi chimene Yehova komanso Yesu anatisonyeza.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 33

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 116 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena