Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 June tsamba 4
  • June 17-23

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 17-23
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 June tsamba 4

June 17-23

AEFESO 4-6

  • Nyimbo Na. 71 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Valani Zida Zonse Zankhondo Zochokera kwa Mulungu”: (10 min.)

    • Aef. 6:11-13​—Timafunika kutetezedwa kuti Satana ndi ziwanda zake asatigonjetse (w18.05 27 ¶1)

    • Aef. 6:14, 15​—Muzidziteteza ndi choonadi, chilungamo komanso uthenga wabwino wamtendere (w18.05 28-29 ¶4, 7, 10)

    • Aef. 6:16, 17​—Muzidziteteza ndi chikhulupiriro, chiyembekezo cha chipulumutso komanso Mawu a Mulungu (w18.05 29-31 ¶13, 16, 20)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Aef. 4:30​—Kodi munthu angamvetse bwanji chisoni mzimu woyera wa Mulungu? (it-1 1128 ¶3)

    • Aef. 5:5​—Kodi munthu waumbombo amakhala bwanji wopembedza mafano? (it-1 1006 ¶2)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aef. 4:17-32 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 6)

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulaliki. Musonyezeni ndi kukambirana mfundo za m’vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? (koma musaonetse vidiyoyi) (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 135

  • “Kodi Maganizo a Yehova Ndi Otani pa Nkhaniyi?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Pitirizani Kuzindikira Chifuniro cha Yehova (Lev. 19:18).

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 40

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 106 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena