September 23-29
AHEBERI 12-13
Nyimbo Na. 88 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Chilango Chimasonyeza Kuti Yehova Amatikonda”: (10 min.)
Aheb. 12:5—Mukapatsidwa chilango, musamakhumudwe n’kusiya kuchita zoyenera (w12 3/15 29 ¶18)
Aheb. 12:6, 7—Yehova amalanga anthu amene amawakonda (w12 7/1 21 ¶3)
Aheb. 12:11—Ngakhale kuti chilango ndi chowawa, chimatithandiza kuti tikhale anthu abwino (w18.03 32 ¶18)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Aheb. 12:1—Kodi chitsanzo cha ‘mtambo waukulu wa mboni’ chimatilimbikitsa bwanji? (w11 9/15 17-18 ¶11)
Aheb. 13:9—Kodi vesili limatanthauza chiyani? (w89 12/15 22 ¶10)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aheb. 12:1-17 (th phunziro 11)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 2)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) lvs 39-40 ¶19 (th phunziro 6)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Tizikhalabe Okhulupirika . . . Ngakhale Kuti si Ife Angwiro: (5 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa:
Kodi M’bale Cázares wakhala akulimbana ndi vuto lotani kungochokera pamene anayamba kutumikira Yehova?
Kodi m’baleyu anathandizidwa bwanji?
Zofunika Pampingo: (10 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 52
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 93 ndi Pemphero