September 30–October 6
YAKOBO 1-2
Nyimbo Na. 122 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kuganizira Zoipa N’koopsa”: (10 min.)
[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yakobo.]
Yak. 1:14—Kuganizira zolakwika kumachititsa kuti munthu ayambe kulakalaka zoipa (g17.4 14)
Yak. 1:15—Kulakalaka zoipa kungachititse kuti munthu achite tchimo lomwe pamapeto pake limabweretsa imfa (g17.4 14)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Yak. 1:17—N’chifukwa chiyani Yehova amatchedwa “Atate wa zounikira zonse zakuthambo”? (it-2 253-254)
Yak. 2:8—Kodi “lamulo lachifumu” n’chiyani? (it-2 222 ¶4)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yak. 2:10-26 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse. Muitanireni kumisonkhano yathu. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 4 min.) Sankhani lemba lililonse. M’patseni buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu. (th phunziro 12)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) bhs 30 ¶4-5 (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Pitirizani Kuganizira Zimenezi”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzipewa Zinthu Zimene Zingawononge Khalidwe Lanu la Kukhulupirika—Zosangalatsa Zosayenera.
Makolo, Muzithandiza Ana Anu Kudziwa Kuopsa Kotumizirana Zinthu Zolaula: (7 min.) Nkhani yokambidwa ndi mkulu, yochokera mu Galamukani! ya November 2013 tsamba 4-5.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 53
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 142 ndi Pemphero