Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 November tsamba 2
  • November 4-10

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 4-10
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 November tsamba 2

November 4-10

1 YOHANE 1-5

  • Nyimbo Na. 122 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Musamakonde Dziko Kapena Zinthu za M’dziko”: (10 min.)

    • [Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 1 Yohane.]

    • 1 Yoh. 2:15, 16​—“Chilichonse cha m’dziko . . . sizichokera kwa Atate, koma kudziko” (w05 1/1 10 ¶13)

    • 1 Yoh. 2:17​—Dziko likupita limodzi ndi chilakolako chake (w13 8/15 27 ¶18)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • 1 Yoh. 2:7, 8​—Kodi lamulo limene Yohane analitchula limakhala bwanji lakale komanso latsopano? (w13 9/15 10 ¶14)

    • 1 Yoh. 5:16, 17​—Kodi ndi tchimo liti limene ndi “lobweretsa imfa”? (it-1 862 ¶5)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 1 Yoh. 1:1–2:6 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kulankhula ndi Mtima Wonse, kenako kambiranani phunziro 11 m’kabuku ka Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w04 10/1 29​—Mutu: Kodi Yohane Ankatanthauza Chiyani pa 1 Yohane 4:18, Pamene Ananena Kuti “Chikondi Chimene Chili Chokwanira Chimathetsa Mantha”? (th Phunziro 7)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 132

  • “Musamatengere Maganizo a M’dzikoli Mukamakonzekera Ukwati”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ukwati Umene Umalemekeza Yehova.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 58

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 34 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena