Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 December tsamba 5
  • December 23-29

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 23-29
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 December tsamba 5

December 23-29

CHIVUMBULUTSO 17-19

  • Nyimbo Na. 149 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Nkhondo ya Mulungu Idzathetsa Nkhondo Zonse”: (10 min.)

    • Chiv. 19:11, 14-16​—Khristu Yesu adzapereka chiweruzo cha Mulungu cholungama (w08 4/1 8 ¶3-4; it-1 1146 ¶1)

    • Chiv. 19:19, 20​—Chilombo ndi mneneri wonyenga zidzawonongedwa (re 286 ¶24)

    • Chiv. 19:21​—Anthu onse omwe amatsutsa ulamuliro wa Mulungu adzawonongedwa (re 286 ¶25)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Chiv. 17:8​—Fotokozani tanthauzo la mawu akuti “chilombocho chinalipo, tsopano palibe, komabe chidzakhalapo.” (re 247-248 ¶5-6)

    • Chiv. 17:16, 17​—Kodi timadziwa bwanji kuti zipembedzo zonyenga sizidzatha zokha? (w12 6/15 18 ¶17)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Chiv. 17:1-11 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 8)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) jl phunziro 8 (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 150

  • Ndithandizeni Ndikhale Wolimba Mtima: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya nyimbo yakuti Ndithandizeni Ndikhale Wolimba Mtima. Kenako kambiranani mafunso awa: Kodi pa moyo wathu timakumana ndi zinthu ziti zomwe zimafunika kulimba mtima? Kodi ndi nkhani za m’Baibulo ziti zomwe zimakulimbikitsani? Kodi ndi ndani amene amatithandiza? Pomaliza, pemphani onse kuti aimirire kuti muimbe nyimbo yakuti “Ndithandizeni Ndikhale Wolimba Mtima” (ya pamisonkhano).

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 65

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 65 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena