Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 January tsamba 6
  • January 27–February 2

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 27–February 2
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 January tsamba 6

January 27–February 2

GENESIS 9-11

  • Nyimbo Na. 101 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Dziko Lonse Lapansi Linali ndi Chilankhulo Chimodzi”: (10 min.)

    • Gen. 11:1-4​—Anthu ena anayamba kumanga mzinda ndi nsanja motsutsana ndi cholinga cha Mulungu (it-1 239; it-2 202 ¶2)

    • Gen. 11:6-8​—Yehova anasokoneza chilankhulo chawo (it-2 202 ¶3)

    • Gen. 11:9​—Anthuwo anasiya kumanga ndipo anabalalikira mbali zosiyanasiyana (it-2 472)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Gen. 9:20-22, 24, 25​—N’chifukwa chiyani Nowa anatemberera Kanani m’malo mwa Hamu? (it-1 1023 ¶4)

    • Gen. 10:9, 10​—Kodi Nimurodi anakhala bwanji “mlenje wamphamvu wotsutsana ndi Yehova”? (it-2 503)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Gen. 10:6-32 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ndipo kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: N’chiyani chikusonyeza kuti ofalitsawa anali limodzi pamene amakonzekera ulendo wobwerezawu? Kodi m’bale uja anachita chiyani kuti asonyeze mwininyumba chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira n’kuyambitsa phunziro la Baibulo?

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 4)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri, kenako yambani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito buku la Zimene Baibulo Limaphunzitsa. (th phunziro 2)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 60

  • “Muzigwira Ntchito Yanu Mwaluso”: (15 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi woyang’anira utumiki.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 70

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 144 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena