February 3-9
GENESIS 12-14
Nyimbo Na. 14 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Pangano Lomwe Limakukhudzani”: (10 min.)
Gen. 12:1, 2—Yehova analonjeza kuti adzadalitsa Abulamu (Abulahamu) (it-1 522 ¶4)
Gen. 12:3—“Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso chifukwa cha [Abulahamu]” (w89 7/1 3 ¶4)
Gen. 13:14-17—Yehova anaonetsa Abulahamu dziko limene anadzalipereka kwa ana ake (it-2 213 ¶3)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Gen. 13:8, 9—Kodi tingatsanzire bwanji Abulahamu pa nkhani yopewa mikangano? (w16.05 5 ¶12)
Gen. 14:18-20—Kodi Levi “anapereka zakhumi” kudzera mwa Abulahamu m’njira yotani? (Ahe 7:4-10; it-2 683 ¶1)
Kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Gen. 12:1-20 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kuthandiza Anthu Kuti Aone Mfundo Zazikulu, kenako kambiranani phunziro 14 m’kabuku ka Kuphunzitsa.
Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w12 1/1 8—Mutu: N’chifukwa Chiyani Tinganene Kuti Sara Anali Mkazi Wabwino Kwambiri? (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na 144
“Kodi Tingaphunzire Chiyani Kuchokera mu Nyimbo za Broadcasting?”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yanyimbo yakuti Dziko Latsopano Lili Pafupi.
Zofunika Pampingo: (5 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 71
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 34 ndi Pemphero