Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 June tsamba 3
  • June 8-14

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 8-14
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 June tsamba 3

June 8-14

GENESIS 46-47

  • Nyimbo Na. 86 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Chakudya pa Nthawi ya Njala”: (10 min.)

    • Gen. 47:13​—Ku Iguputo ndi ku Kanani kunagwa njala yaikulu (w87 5/1 15 ¶2)

    • Gen. 47:16, 19, 20​—Aiguputo analolera kusiya zinthu zawo kuti akhale ndi moyo

    • Gen. 47:23-25​—Pamafunika khama kuti tizipindula ndi chakudya chauzimu chomwe tili nacho (kr 234-235 ¶11-12)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Gen. 46:4​—Kodi zimene Yakobo anauzidwa kuti Yosefe ndi amene ‘adzamutseke maso’ zinkatanthauza chiyani? (it-1 220 ¶1)

    • Gen. 46:26, 27​—Kodi ndi anthu angati a m’banja la Yakobo omwe anakalowa m’dziko la Iguputo? (nwtsty mfundo zophunzirira, Mac. 7:14)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Gen. 47:1-17 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi wofalitsayu anagwiritsa ntchito bwanji mafunso mwaluso? Nanga anafotokoza bwanji lemba m’njira yomveka bwino?

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako gawirani buku kapena magazini yopezeka pa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 3)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako gawirani buku la Zimene Baibulo Limaphunzitsa ndipo yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito mutu 9. (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 96

  • Muzilola Kuti Yehova Azikukumbutsani: (15 min.) Onerani vidiyo yakuti Tiziyamikira Zikumbutso za Yehova. Limbikitsani onse kuti apitirize kuwerenga Mawu a Mulungu komanso kudya chakudya chonse chauzimu chomwe timalandira.​—Yes. 25:6; 55:1; 65:13; Mat. 24:45.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 87

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 39 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena