Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 November tsamba 6
  • Umboni Wakuti Yehova Ankawadalitsa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Umboni Wakuti Yehova Ankawadalitsa
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • “Amatsatira Mwanawankhosa” Nthawi Zonse
    Nsanja ya Olonda—2009
  • “Kapolo” Amene Ali Wokhulupirika ndi Wanzeru
    Nsanja ya Olonda—2004
  • “Ndani Kwenikweni Amene Ali Kapolo Wokhulupirika ndi Wanzeru?”
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Kodi Kapolo Wokhulupirika Ndi Wanzeru Ndani?
    Kodi Ndani Akuchita Chifuniro cha Yehova Masiku Ano?
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 November tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 8-9

Umboni Wakuti Yehova Ankawadalitsa

8:6-9, 12; 9:1-5, 23, 24

Yehova anachititsa kuti moto unyeketse nsembe yopsereza yoyambirira imene ansembe atsopano a m’banja la Aroni anapereka. Zimenezi zinasonyeza kuti Yehova ankathandiza komanso kuvomereza ansembewo. Pamenepa Yehova analimbikitsa Aisiraeli onse amene ankaona zinthuzi zikuchitika kuti azilemekeza ansembewo. Masiku ano, Yehova akugwiritsa ntchito Yesu Khristu monga Mkulu wa Ansembe wapamwamba kwambiri. (Ahe 9:11, 12) Mu 1919, Yesu anasankha kagulu ka Akhristu odzozedwa kuti kakhale “kapolo wokhulupirika ndi wanzeru.” (Mt 24:45) Kodi n’chiyani chimasonyeza kuti Yehova amathandiza komanso kuvomereza kapolo wokhulupirikayu?

  • Ngakhale kuti kapolo wokhulupirikayu wakhala akuzunzidwa, akupitirizabe kupereka chakudya chauzimu

  • Mogwirizana ndi ulosi, uthenga wabwino ukulalikidwa “padziko lonse lapansi kumene kuli anthu.”​—Mt 24:14

Kodi tingachite bwanji zinthu mogwirizana ndi kapolo wokhulupirika ndi wanzeru?

1. Yesu wapatsidwa ulemerero ndipo akulamulira dziko lapansi. 2. Kapolo wokhulupirika ndi wanzeru wakumana kuti apereke chakudya chauzimu. 3. M’bale akulalikira uthenga wabwino kwa mzibambo
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena