Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 December tsamba 4
  • December 14-20

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 14-20
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 December tsamba 4

December 14-20

LEVITIKO 12-13

  • Nyimbo Na. 140 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Tingaphunzire pa Malamulo Okhudza Khate”: (10 min.)

    • Le 13:4, 5​—Anthu odwala khate ankaikidwa kwaokha (wp18.1 7)

    • Le 13:45, 46​—Akhate ankayenera kupewa kupatsira ena (wp16.4 9 ¶1)

    • Le 13:52, 57​—Zinthu zimene zadetsedwa zinkafunika kuwonongedwa (it-2 238 ¶3)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 12:2, 5​—N’chifukwa chiyani mayi ankakhala wodetsedwa akabereka mwana? (w04 5/15 23 ¶2)

    • Le 12:3​—Kodi n’chiyani chimene chiyenera kuti chinachititsa Yehova kulamula kuti ana aamuna azidulidwa akakwanitsa masiku 8 atabadwa? (wp18.1 7)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 13:9-28 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (4 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso akuti: Kodi Tony anagwiritsa ntchito bwanji mafunso mwanzeru? Kodi anathandiza bwanji munthuyo kumvetsa mfundo yamulembalo?

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 19)

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako musonyezeni kabuku ka Uthenga Wabwino n’kuyamba kuphunzira naye phunziro 11. (th phunziro 9)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 125

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 112

  • Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 143 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena