Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 December tsamba 5
  • December 21-27

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 21-27
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 December tsamba 5

December 21-27

LEVITIKO 14-15

  • Nyimbo Na. 122 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Timafunika Kukhala Oyera Kuti Tizilambira Mulungu Movomerezeka”: (10 min.)

    • Le 15:13-15​—Amuna ankafunika kudziyeretsa akadetsedwa (it-1 263)

    • Le 15:28-30​—Akazi ankafunika kudziyeretsa akadetsedwa (it-2 372 ¶2)

    • Le 15:31​—Yehova amafuna kuti anthu amene amamulambira azikhala oyera (it-1 1133)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 14:14, 17, 25, 28​—Kodi tingaphunzire chiyani pa zimene wakhate ankafunika kuchita kuti akhale woyera? (it-1 665 ¶5)

    • Le 14:43-45​—Kodi lamulo lokhudza khate loopsa m’nyumba linkaphunzitsa Aisiraeli mfundo iti yokhudza Yehova? (g 1/06 14, bokosi)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 14:1-18 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako perekani magazini yokhudza nkhani imene mwininyumbayo anayambitsa. (th phunziro 16

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi a Mboni za Yehova ndi Anthu Otani? kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyi. (th phunziro 11)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) fg phunziro 11 ¶6-7 (th phunziro 19)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 76

  • “Tizigwiritsabe Ntchito Magazini”: (10 min.) Nkhani yokambirana.

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (5 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 113

  • Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 84 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena