Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsamba 15
  • February 22-28

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 22-28
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 January tsamba 15

February 22-28

NUMERI 5–6

  • Nyimbo Na. 81 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mungatsanzire Bwanji Anaziri?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 6:​6, 7​—Kodi zinatheka bwanji kuti Samisoni agwire mitembo ya anthu amene anapha koma n’kupitirizabe kukhala Mnaziri? (w05 1/15 30 ¶2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 5:​1-18 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi a Mboni za Yehova ndi Anthu Otani? ndipo kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 3)

  • Nkhani: (5 min.) w06 1/15 32​—Mutu: Zinthu Zimene Akatswiri Anapeza Zomwe Zimasonyeza Kuti Baibulo Ndi Lolondola. (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 76

  • “Kodi Mudzachita Upainiya Wothandiza M’mwezi wa March Kapena April?” (5 min.) Nkhani yokambirana.

  • Ntchito Yoitanira Anthu ku Chikumbutso Idzayamba Loweruka pa 27 February: (10 min.) Nkhani yokambirana. Perekani kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso kwa aliyense n’kukambirana mwachidule mfundo zake. Fotokozani zimene mpingo wanu wakonza kuti mudzakwanitse kuitanira anthu onse a m’gawo lanu. Onerani vidiyo ya zimene tinganene pogawira kapepalaka. Funsani omvera kuti: Kodi ndi nthawiiti pamene tiyenera kumuonetsa mwininyumba vidiyo yakuti, Tizikumbukira Imfa ya Yesu? Kodi mwininyumba angasonyeze chidwi m’njira ziti?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 122

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 42 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena