Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsamba 2
  • March 1-7

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 1-7
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 March tsamba 2

March 1-7

NUMERI 7–8

  • Nyimbo Na. 4 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Tingaphunzire pa Zomwe Zinkachitika pa Msasa wa Aisiraeli”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 8:17​—Kodi Yehova ankawaona bwanji ana aamuna oyamba kubadwa a mu Isiraeli? (it-1 835)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 7:1-17 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene poitanira anthu ku Chikumbutso. (th phunziro 11)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. (th phunziro 6)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Itanirani ku Chikumbutso munthu amene munkaphunzira naye Baibulo. (th phunziro 12)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Itanirani ku Chikumbutso wachibale amene munamulalikirapo m’mbuyomu. (th phunziro 17)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 54

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (5 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya March.

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 123 ndi bokosi lakuti “Thukuta la Yesu Linaoneka Ngati Madontho a Magazi.”

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 44 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena