Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsamba 10
  • April 5-11

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 5-11
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 March tsamba 10

April 5-11

NUMERI 17-19

  • Nyimbo Na. 80 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Ine Ndine . . . Cholowa Chako”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 18:19; mawu a m’munsi.​—Kodi mawu akuti “pangano losatha la mchere” akutanthauza chiyani? (g02 6/8 14 ¶2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 18:1-13 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (4 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Wobwereza: Yesu​—Mt 20:28. Muziimitsa nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Musonyezeni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 6)

  • Nkhani: (5 min.) w18.01 18 ¶4-6​—Mutu: N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupereka kwa Yehova? (th phunziro 20)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 117

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 128

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 14 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena