Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsamba 12
  • April 19-25

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 19-25
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 March tsamba 12

April 19-25

NUMERI 22-24

  • Nyimbo Na. 8 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Amasintha Temberero N’kukhala Dalitso”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 22:20-22​—N’chifukwa chiyani Yehova anakwiyira kwambiri Balamu? (w04 8/1 27 ¶2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 23:11-26 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • “Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki​—Muzigwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa​—Muzigwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu.

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) fg phunziro 5 ¶3-4 (th phunziro 6)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 38

  • “Yehova Amasintha Chizunzo N’kukhala Mwayi Wolalikira”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kucheza ndi Dmitriy Mikhaylov.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 130

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 15 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena