Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsamba 14
  • April 26–May 2

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 26–May 2
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 March tsamba 14

April 26–May 2

NUMERI 25-26

  • Nyimbo Na. 135 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Zochita za Munthu Mmodzi Zingasinthe Zinthu?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 26:55, 56​—Kodi mmene Yehova anagawira cholowa cha malo ku mafuko a Aisiraeli zinasonyeza bwanji kuti ndi wanzeru? (it-1 359 ¶1-2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 25:1-18 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo ndipo kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyo. (th phunziro 3)

  • Nkhani (5 min.) w04 4/1 29​—Mutu: N’chifukwa Chiyani Chiwerengero Chomwe Chili pa Numeri 25:9 Chimasiyana ndi cha pa 1 Akorinto 10:8? (th phunziro 17)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 28

  • “Muzisankha Anzanu Mwanzeru”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani mbali ya vidiyo yakuti Zitsanzo Zotichenjeza Masiku Ano.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 131

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 145 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena