Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsamba 3
  • May 10-16

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 10-16
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 May tsamba 3

May 10-16

NUMERI 30-31

  • Nyimbo Na. 51 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzikwaniritsa Zimene Mwalonjeza”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 30:10-12​—Kodi tikudziwa bwanji kuti Elikana anavomereza zimene Hana analonjeza kuti adzapereka Samueli kwa Yehova kuti azimutumikira? (1Sa 1:11; it-2 28 ¶1)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 30:1-16 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Wobwereza: Cholinga cha Mulungu​—Yes 55:11. Muziimitsa nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 6)

  • Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu, ndipo kenako yambitsani phunziro la Baibulo. (th phunziro 19)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 5

  • Tingaphunzire Kupirira Kuchokera ku Zinthu za M’chilengedwe: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa pa chomera komanso nyama iliyonse imene yasonyezedwa m’vidiyoyi. Kodi cholengedwa chimenechi chikutiphunzitsa chiyani pa nkhani ya kupirira? Monga Akhristu, kodi tingasonyeze bwanji kupirira kofanana ndi kwa cholengedwachi pa moyo wathu?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 133

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 46 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena