Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsamba 4
  • May 17-23

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 17-23
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 May tsamba 4

May 17-23

NUMERI 32-33

  • Nyimbo Na. 142 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mukathamangitse Anthu Onse a M’dzikolo”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 33:54​—Kodi malo ankagawidwa bwanji ku mafuko a Aisiraeli? (it-1 359 ¶2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 32:28-42 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • “Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki​—Muzigwiritsa Ntchito Mafanizo”: (10 min.) Nkhani Yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa​—Muzigwiritsa Ntchito Mafanizo.

  • Nkhani: (5 min.) w09 10/1 30, bokosi​—Mutu: N’chifukwa Chiyani Yehova Ankadalitsa Nkhondo Zimene Aisiraeli Akale Ankamenya? (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 58

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 134

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena