Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsamba 8
  • May 31–June 6

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 31–June 6
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 May tsamba 8

May 31–June 6

DEUTERONOMO 1–2

  • Nyimbo Na. 125 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mukuweruzira Mulungu”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • De 1:19; 2:7​—Kodi Yehova anasamalira bwanji anthu ake pa zaka 40 zimene ankayenda ‘m’chipululu chachikulu ndi chochititsa mantha’? (w13 9/15 9 ¶9)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 1:1-18 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 16)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni kapepala koitanira anthu kumisonkhano yathu, ndipo kenako yerekezani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? (th phunziro 11)

  • Nkhani: (5 min.) w13 8/15 11 ¶7​—Mutu: Muzipewa Kulankhula Kapena Kumvetsera Nkhani Zoipa. (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 30

  • “Khalanibe Okonzeka Pamene Tili Kumapeto kwa ‘Masiku Otsiriza’”: (15 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi mkulu. Onerani vidiyo yakuti Zimene Tingachite Pokonzekera Masoka Achilengedwe. Tchulaninso zilengezo zochokera ku ofesi ya nthambi kapena ku bungwe la akulu ngati zilipo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 136

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena