June 21-27
DEUTERONOMO 7-8
Nyimbo Na. 136 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Usadzachite Nawo Mgwirizano wa Ukwati”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
De 8:3—Kodi tingaphunzire chiyani pa mana amene Yehova ankapatsa Aisiraeli? (w04 2/1 13 ¶4)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 7:1-16 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Muitanireni kumisonkhano yathu. (th phunziro 15)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 9)
Nkhani: (5 min.) w06 1/1 28 ¶14-15—Mutu: Musaiwale Yehova. (th phunziro 7)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 35
Zimene Gulu Lathu Lachita: (5 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya June.
Zofunika Pampingo: (10 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 139 ndi bokosi lakuti “Kuti Mutsanzire Yesu Muyenera . . . ”
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 139 ndi Pemphero